14 Ndipo Hezekiya analandira kalatayo ku dzanja la mithenga, namwerenga, nakwera Hezekiya kumka ku nyumba ya Yehova, namfunyulula pamaso pa Yehova.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19
Onani 2 Mafumu 19:14 nkhani