3 Nati kwa iye, Atero Hezekiya, Lero line ndilo tsiku la cisautso, ndi la kudzudzula, ndi la kunyoza; pakuti ana anafikira kubadwa, koma palibe mphamvu yakubala.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19
Onani 2 Mafumu 19:3 nkhani