7 Taonani, ndidzalonga mwa iye mzimu wakuti adzamva mbiri, nadzabwerera kumka ku dziko lace, ndipo ndidzamgwetsa ndi lupanga m'dziko lace.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19
Onani 2 Mafumu 19:7 nkhani