9 Ndipo anamva za Tirihaka mfumu ya Kusi, akuti, Taonani, waturuka kuthirana nawe nkhondo. Pamenepo anatumizanso mithenga kwa Hezekiya, ndi kuti,
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19
Onani 2 Mafumu 19:9 nkhani