2 Mafumu 2:24 BL92

24 Ndipo anaceuka, nawaona, nawatemberera m'dzina la Yehova. Ndipo kuthengo kunaturuka zimbalangondo ziwiri zazikazi, ndi kupwetedza mwa iwo ana makumi anai mphambu awiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:24 nkhani