2 Mafumu 20:15 BL92

15 Nati iye, Anaona ciani m'nyumba mwanu? Nati Hezekiya, Zonse za m'nyumba mwanga anaziona, palibe kanthu pacuma canga kosawaonetsa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 20

Onani 2 Mafumu 20:15 nkhani