2 Mafumu 21:16 BL92

16 Ndiponso Manase anakhetsa mwazi wambiri wosacimwa mpaka anadzaza m'Yerusalemu monsemo, osawerenga kulakwa kwace analakwitsa nako Yuda, ndi kucita coipa pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 21

Onani 2 Mafumu 21:16 nkhani