17 popeza anandisiya Ine, nafukizira zonunkhira milungu yina, kuti autse mkwiyo wanga ndi nchito zonse za manja ao; cifukwa cace mkwiyo wanga udzayakira malo ana wosazimikanso.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 22
Onani 2 Mafumu 22:17 nkhani