2 Mafumu 22:4 BL92

4 Kwera kwa Hilikiya mkulu wa ansembe, awerenge ndalama zimene anthu anabwera nazo ku nyumba ya Yehova, ndizo zimene olindira pakhomo anasonkhetsa anthu; azipereke m'dzanja anchito akuyang'anira nyumba ya Yehova;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 22

Onani 2 Mafumu 22:4 nkhani