2 Mafumu 23:15 BL92

15 Anagumulanso guwa la nsembe linali ku Beteli, ndi msanje adaumanga Yerobiamu mwana wa Nebati wolakwitsa Israyeli uja; guwa la nsembelo, ndi msanje womwe anagumula; natentha msanje, naupondereza ukhale pfumbi, natentha cifanizoco.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:15 nkhani