2 Mafumu 23:18 BL92

18 Nati iye, Mlekeni, munthu asakhudze mafupa ace. Naleka iwo mafupa ace akhale pamodzi ndi mafupa a mneneri uja anaturuka m'Samariya.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:18 nkhani