2 Mafumu 23:23 BL92

23 koma Paskha ili analicitira Yehova m'Yerusalemu, Yosiya atakhala mfumu zaka khumi mphambu zisanu ndi zitatu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:23 nkhani