2 Mafumu 23:29 BL92

29 Masiku ace Farao-Neko mfumu ya Aigupto anakwerera mfumu ya Asuri ku mtsinje wa Firate; Ddipo mfumu Yosiya anaturuka kuponyana naye, koma anapha Yosiya ku Megido, atamuona.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:29 nkhani