2 Mafumu 23:3 BL92

3 Niima mfumu paciunda, nicita pangano pamaso pa Yehova, kutsata Yehova, ndi kusunga malamulo ace, ndi mboni zace, ndi malemba ace, ndi mtima wonse ndi moyo wonse, kukhazikitsa mau a cipangano colembedwa m'buku ili; ndipo anthu onse anaimiririra panganoli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:3 nkhani