2 Mafumu 23:33 BL92

33 Ndipo Faraoneko anammanga m'Ribila, m'dziko la Hamati; kuti asacite ufumu m'Yerusalemu; nasonkhetsa dzikoli msonkho wa matalente zana limodzi la siliva, ndi talente limodzi la golidi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:33 nkhani