2 Mafumu 23:36 BL92

36 Yoyakimu anali wa zaka makumi awiri ndi zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka khumi ndi cimodzi m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Zebida mwana wa Pedaya wa Ruma.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:36 nkhani