2 Mafumu 23:7 BL92

7 Nagamula nyumba za anyamata adama okhala ku nyumba ya Yehova, kumene akazi anaomba nsaru zolenjeka za cifanizoco.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:7 nkhani