2 Mafumu 24:2 BL92

2 Ndipo Yehova anamtumizira magulu a Akasidi, ndi magulu a Aaramu, ndi magulu a Amoabu, ndi magulu a ana a Amoni, nawatumiza pa Yuda kuliononga, monga mwa mau a Yehova: adawanena ndi dzanja la atumiki ace aneneriwo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:2 nkhani