2 Mafumu 24:4 BL92

4 ndiponso cifukwa ca mwazi wosacimwa adaukhetsa; popeza anadzaza Yerusalemu ndi mwazi wosacimwa; ndipo Yehova sanafuna kukhululukira.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:4 nkhani