2 Mafumu 25:22 BL92

22 Koma kunena za anthu otsalira m'dziko la Yuda, amene adawasiya Nebukadinezara mfumu ya Babulo, iyeyu anamuika Gedaliya mwana wa Ahikamu mwana wa Safani akhale wowalamulira.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25

Onani 2 Mafumu 25:22 nkhani