2 Mafumu 25:25 BL92

25 Koma kunali mwezi wacisanu ndi ciwiri anadza Ismayeli mwana wa Netaniya mwana wa Elisama, wa mbumba yacifumu, ndi anthu khumi pamodzi naye, nakantha Gedaliya; nafa iye, ndi Ayuda, ndi Akasidi okhala naye ku Mizipa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25

Onani 2 Mafumu 25:25 nkhani