2 Mafumu 25:30 BL92

30 Ndi kunena za cakudya cace, panali cakudya cosalekeza copatsidwa kwa iye ndi mfumu, tsiku Uri lonse gawo lace, masiku onse a moyo wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25

Onani 2 Mafumu 25:30 nkhani