2 Mafumu 25:7 BL92

7 Napha ana a Zedekiya pamaso pace, namkolowola Zedekiya maso ace, nammanga ndi maunyolo amkuwa, namuka nave ku Babulo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25

Onani 2 Mafumu 25:7 nkhani