2 Mafumu 25:9 BL92

9 natentha nyumba ya Yehova, ndi nyumba ya mfumu, ndi nyumba zonse za m'Yerusalemu; ndi nyumba zonse zazikuru anazitentha ndi moto.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25

Onani 2 Mafumu 25:9 nkhani