2 Mafumu 3:14 BL92

14 Ndipo Elisa anati, Pali Yehova wa makamu, amene ndiima pamaso pace, ndikadapanda kusamalira nkhope ya Yehosafati mfumu ya Yuda, sindikadakuyang'anitsani, kapena kukuonani.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:14 nkhani