2 Mafumu 3:19 BL92

19 Ndipo mudzakantha midzi yonse ya matioga, ndi midzi yonse yosankhika, ndi kulikha mitengo yonse yabwino, ndi kufotsera zitsime zonse zamadzi, ndi kuipitsa pa nthaka ponse pabwino ndi miyala.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:19 nkhani