2 Mafumu 3:21 BL92

21 Atamva tsono Amoabu onse kuti adakwera mafumu aja kuthirana nao nkhondo, anamemeza onse akumanga lamba m'cuuno ndi okulapo, naima iwo m'malire.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:21 nkhani