2 Mafumu 3:24 BL92

24 Ndipo pamene anafika ku misasa ya Israyeli, Aisrayeli ananyamuka, nakantha Amoabu, nathawa iwo pamaso pao; ndipo analowa m'dziko ndi kukantha Amoabu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:24 nkhani