2 Mafumu 4:25 BL92

25 Potero anamuka, nafika kwa munthu wa Mulungu ku phiri la Karimeli. Ndipo kunali, pakumuona munthu wa Mulungu alinkudza kutali, anati kwa Gehazi mnyamata wace, Tapenya, suyo Msunemu uja;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:25 nkhani