2 Mafumu 4:31 BL92

31 Nawatsogolera Gehazi, naika ndodo pankhope pa mwanayo; koma mwanayo analibe mau, kapena kusamalira. Motero anabwerera kukomana naye, namuuza kuti, Sanauke mwanayo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:31 nkhani