2 Mafumu 4:36 BL92

36 Pamenepo anaitana Gehazi, nati, Kaitane Msunemu uja, Namuitana. Ndipo atalowa kuli iye, anati, Nyamula mwana wako.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:36 nkhani