2 Mafumu 4:43 BL92

43 Koma mnyamata wace anati, Ciani? ndigawire amuna zana ici kodi? Koma anati, Uwapatse anthu kuti adye; pakuti atero Yehova, Adzadya nadzasivako.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:43 nkhani