2 Mafumu 4:6 BL92

6 Ndipo kunali, zitadzala zotengera, anati kwa mwana wace, Nditengere cotengera cina, Nanena naye, Palibe cotengera cina. Ndipo mafuta analeka.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:6 nkhani