2 Mafumu 4:8 BL92

8 Ndipo linafika tsiku lakuti Elisa anapitirira kumka ku Sunemu, kumeneko kunali mkazi womveka; ameneyo anamuumiriza adye mkate. Potero pomapitirako iyeyu, adafowapa, mbukirako kukadya mkate.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:8 nkhani