2 Mafumu 5:1 BL92

1 Ndipo Namani kazembe wa khamu la nkhondo la mfumu ya Aramu anali munthu womveka pamaso pa mbuyace, ndi waulemu; popeza mwa iye Yehova adapulumutsa Aaramu; ndiyenso ngwazi, koma wakhate.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:1 nkhani