13 Pamenepo anyamata ace anasendera, nanena naye, nati, Atate wanga, mneneri akadakuuzani cinthu cacikuru, simukadacicita kodi? koposa kotani nanga ponena iye, Samba, nukonzeke?
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5
Onani 2 Mafumu 5:13 nkhani