2 Mafumu 5:21 BL92

21 Motero Gehazi anatsata Namani. Ndipo pamene Namani anaona wina alikumthamangira, anatsika pagareta kukomana naye, nati, Nkwabwino kodi?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:21 nkhani