2 Mafumu 5:3 BL92

3 Nati uyu kwa mbuyace wamkazi, Mbuye wanga akadakhala kwa mneneri ali m'Samariya, akadamciritsa khate lace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:3 nkhani