2 Mafumu 6:18 BL92

18 Ndipo atatsikira pali iye, Elisa anapemphera kwa Yehova, nati, Mukanthe mtundu uwu ucite khungu. Ndipo iye anawakantha, nawacititsa khungu, monga mwa mau a Elisa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6

Onani 2 Mafumu 6:18 nkhani