2 Mafumu 6:20 BL92

20 Ndipo kunali, pakufika ku Samariya, Elisa anati, Yehova, muwakanganulire awa maso kuti aone. Nawakanganulira Yehova maso ao, naona iwo, ndipo tapenyani, ali pakati pa Samariya.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6

Onani 2 Mafumu 6:20 nkhani