2 Mafumu 6:25 BL92

25 Koma m'Samariya munali njala yaikuru; ndipo taonani, anaumangira misasa mpaka mutu wa buru unagulidwa ndalama zasiliva makumi asanu ndi atatu; ndi limodzi la magawo anai la muyeso wa zitosi za nkhunda linagulidwa ndi ndalama zasiliva zisanu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6

Onani 2 Mafumu 6:25 nkhani