2 Mafumu 6:6 BL92

6 Nati munthu wa Mulungu, Yagwera pati? Namuonetsapo yagwera. Pamenepo anadula kamtengo, nakaponya pomwepo, nayandamitsa nkhwangwayo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6

Onani 2 Mafumu 6:6 nkhani