2 Mafumu 8:19 BL92

19 Koma Yehova sanafuna kuononga Yuda, cifukwa ca Davide mtumiki wace monga adamuuza, kuti adzampatsa nyali ya kwa ana ace kosalekeza.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:19 nkhani