2 Mafumu 8:24 BL92

24 Nagona Yoramu ndi makolo ace, naikidwa pamodzi ndi makolo ace m'mudzi wa Davide; ndipo Ahaziya mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:24 nkhani