2 Mafumu 8:4 BL92

4 Koma mfumu inalikulankhula ndi Gehazi mnyamata wa munthu wa Mulungu, ndi kuti, Ndifotokozere zazikuru zonse Elisa wazicita.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:4 nkhani