2 Mafumu 8:9 BL92

9 Namuka Hazaeli kukakomana naye, napita naco caufulu, ndico ca zokoma zonse za m'Damasiko, zosenza ngamila makumi anai, nafika naima pamaso pace, nati, Mwana wanu Benihadadi mfumu ya Aramu, wandituma ine kwa inu, ndi kuti, Kodi ndidzacira nthenda iyi?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:9 nkhani