2 Mafumu 9:22 BL92

22 Ndipo kunali, pamene Yoramu anaona Yehu, anari, Mtendere kodi, Yehu? Nati iye, Ngwanji mtendere pokhala cacuruka cigololo ndi nyanga zace za mai wako Yezebeli?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:22 nkhani