2 Mafumu 9:33 BL92

33 Nati iye, Mgwetsereni pansi. Namgwetsera pansi, nuwazikako mwazi wace pakhoma ndi pa akavalo, nampondereza iye pansi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:33 nkhani