6 Nanyamuka, nalowa m'nyumba; ndipo anatsanulira mafutawo pamutu pace, nanena naye, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Ndakudzoza ukhale mfumu ya pa anthu a Yehova, ndiwo Aisrayeli.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9
Onani 2 Mafumu 9:6 nkhani