2 Mafumu 9:8 BL92

8 Popeza nyumba yonse ya Ahabu idzaonongeka, ndipo ndidzalikhira Ahabu ana amuna onse womangika ndi womasuka m'Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:8 nkhani